Motor bike

Njingayi inachita ngozi, inasweka nyali ya ku tsogolo, dashboard ndi ku nyali ya kumbuyo. Ngati munthu angakonzetse yekha adzanipatsa 1.8m koma ngati ndingakinzetse ndekha ndzidzafunapo 2m. Basi chilichonse ndi chabwino bwino. Ndikufuna wa serious basi adzatenge.

MWK2

seller's name'
Name: Lindani
seller phone number
Location: Lilongwe, Central Region
uploaded on
Date: 09 May, 2026

Contact Seller

Product Images

product image 0
Image 1 of 4
product image 1
Image 2 of 4
product image 2
Image 3 of 4
product image 3
Image 4 of 4
Loading recommendations...