Tiyeni tiphuzire kupanga tokha ma casings opangila sausage pamtengo wa 1000 yokha training ikhalapo ma dzulo ano nthawi ya7:00 KO ma so ndikhala ndikuphuzitsa kupanga mkaka wamadzi ochokera ku mkaka wamadzi 650 komaso kupanga soya milk pa mtengo wa550 ndiphuzitsa Ku panga ice cream and yogurt wapure milk aswel wa flour 0880900953 or drop ur numbers kupangani ad
$650