Ndimafuna ma soft Jean descent trousers or ma descent a bho koma a ma 2 thousand Kwacha. Ndimafuna 10 trousers nde taponyani ma photos ku WhatsApp 0880816961 tiwaone. About location tikambirana ku WhatsApp konko.
$2,000