Musapange naye business ndi wokomba uyu
Guys, guys, Chenjerani ndi munthu uyu, ndi mbava, wokumba, ndipo musapange naye business muberedwa, Akumapanga post zinthu izo, koma ndi okumba, zinthuzo alibe, ndipo akumakunamiza kuti wakatumiza zinthuzo ku Speed, or CTS, mkupanga ma receipt abodza, cholinga umtumizire ndarama, & akumapanga AI zinthuzo as if zili ku SPEED, or CTS, musayelekeze , kupangaa naye business, muberedwa, ndi mbava..
Price: FREE
Private Seller: Denzel K.