
Maize rice for sale in phalombe 50 kg of
Chimanga chabwino chochititsa nkhaso kwambiri ndikugulitsa pa ntengo yosabola nthumba 50 kg ndikugulitsa pa ntengo wa 23500 yokha coz chimanga changa chilibe nakafumbwe ndi chabwino kwambiri komanso ndiri ndi mpunga wa killombero ndipo ndikugulitsa pa 1 kg 740 komanso Pali mbewu dzina monga nyemba ntedza soya ndi nandolo wa serious ayimbe pa 0883102017 iri pa WhatsApp ndimapezeka ku chilinga phalombe Malawi,
Price: $23,500
Private Seller: Grolia M